Qur'an ya Chichewa / Chinyanja offline ikupezeka tsopano pa internet.
Ili ndi ndemanga pansi apo ndi apo.
Ndipo theka la Qur'an imeneyi lili mu Chinyanja / Chichewa chokhachokha, pomwe theka linali lili ndi Arab pansi pa Chichewa / Chinyanja.
Izi zachitika Pofuna kuthandiza ma Daiy omwe akupanga Dakwah mma media sosial komanso awo omwe sabva Arab.
Ndipo kwa opanga Da'wa pa masamba a mchezo yafewetsedwa motere:
Ndiyotheka kuipanga copy and paste kuti pasakhale kulemba chimodzichimodzi. (Klik lama untuk menyalin dan menampal)
Komanso mutha kumutumizira munthu wina app imeneyi kudzera mkati mwa App yomweyi.